Genesis 35:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.* Anamwalira atakhala ndi moyo wautali komanso atakhutira ndi masiku a moyo wake ndipo ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika mʼmanda.+
29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.* Anamwalira atakhala ndi moyo wautali komanso atakhutira ndi masiku a moyo wake ndipo ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika mʼmanda.+