Genesis 35:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake. Anamwalira ali wokalamba, wokhutira ndi masiku ake.+ Ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika m’manda.+
29 Kenako Isaki anamwalira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake. Anamwalira ali wokalamba, wokhutira ndi masiku ake.+ Ana ake, Esau ndi Yakobo, anamuika m’manda.+