Genesis 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+ 1 Mbiri 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamapeto pake, iye anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino ndi wautali,+ wokhutira ndi masiku, chuma+ ndi ulemerero.+ Kenako Solomo mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+
8 Kenako, Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali ndi wokhutira, ndipo anaikidwa m’manda n’kugona ndi makolo ake.+
28 Pamapeto pake, iye anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino ndi wautali,+ wokhutira ndi masiku, chuma+ ndi ulemerero.+ Kenako Solomo mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.+