1 Mafumu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mfumu Davide anali atakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zovala koma sankamva kutentha. Miyambo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Imvi ndizo chisoti chachifumu cha ulemerero+ zikapezeka m’njira yachilungamo.+
1 Mfumu Davide anali atakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zovala koma sankamva kutentha.