Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano si iyi mfumu ikuyenda patsogolo panu!+ Koma ine, ndakalamba+ ndipo ndachita imvi.+ Ana anga aamuna, si awa ali pakati panu,+ ndipo ine ndatumikira Mulungu ndi kukutsogolerani kuyambira pa ubwana wanga, mpaka lero.+

  • Salimo 71:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+

      Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+

      Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+

  • Salimo 92:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zinthu zidzapitiriza kuwayendera bwino ngakhale atachita imvi,+

      Adzakhalabe onenepa ndi athanzi,+

  • Yesaya 46:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena