Salimo 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+ Salimo 116:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ndinaitana pa dzina la Yehova kuti:+“Inu Yehova, pulumutsani moyo wanga!”+
41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+