Salimo 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+ Salimo 89:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.] Salimo 118:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+
41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+
48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.]
25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+