Numeri 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+ 1 Samueli 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.”
17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+
20 Ifenso tikufuna kukhala ngati mitundu ina yonse,+ ndipo mfumu yathuyo ndi imene izitiweruza ndi kutitsogolera kukamenya nkhondo zathu.”