Deuteronomo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+
2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+