Ekisodo 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imene analankhula ndi Farao, Mose anali ndi zaka 80 ndipo Aroni anali ndi zaka 83.+ Deuteronomo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mose anamwalira ali ndi zaka 120.+ Diso lake silinachite mdima+ ndipo anali adakali ndi mphamvu.+ Machitidwe 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsopano pamene anakwanitsa zaka 40 zakubadwa, anaganiza zokayendera abale ake, ana a Isiraeli.+