Deuteronomo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+ Machitidwe 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsopano pamene anakwanitsa zaka 40 zakubadwa, anaganiza zokayendera abale ake, ana a Isiraeli.+ Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai. Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+