Ekisodo 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno pa tsiku limenelo udzauze mwana wako kuti, ‘Ndikuchita izi chifukwa cha zimene Yehova anandichitira potuluka mu Iguputo.’+ 1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+
8 Ndiyeno pa tsiku limenelo udzauze mwana wako kuti, ‘Ndikuchita izi chifukwa cha zimene Yehova anandichitira potuluka mu Iguputo.’+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+