Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+

      Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+

  • Salimo 115:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu ndinu amene mwadalitsidwa ndi Yehova,+

      Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Yesaya 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu woona Yehova, amene analenga kumwamba+ ndiponso Wokutambasula Wamkulu,+ amene anakhazikitsa dziko lapansi+ ndi zonse zimene zili mmenemo,+ amene anapereka mpweya+ kwa anthu amene ali mmenemo,+ ndi mzimu kwa anthu amene amayenda padzikopo,+ iye wanena kuti:

  • Yeremiya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena