Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 136:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yamikani woyala dziko lapansi pamwamba pa madzi:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
6 Yamikani woyala dziko lapansi pamwamba pa madzi:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+