1 Mbiri 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano inu Mulungu wathu, tikukuyamikani+ ndi kutamanda+ dzina lanu lokongola.+ Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+
8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+