Yesaya 63:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Monga momwe chilombo chakutchire chimatsetserekera kuchigwa, mzimu wa Yehova unawapumitsa.”+ Chotero inu munatsogolera anthu anu kuti mudzipangire dzina lokongola.+
14 Monga momwe chilombo chakutchire chimatsetserekera kuchigwa, mzimu wa Yehova unawapumitsa.”+ Chotero inu munatsogolera anthu anu kuti mudzipangire dzina lokongola.+