Levitiko 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova. Yobu 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndinati, ‘Masiku alankhule.Zaka zambiri n’zimene ziyenera kudziwitsa anthu nzeru.’+ Miyambo 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukongola kwa anyamata ndiko mphamvu zawo,+ ndipo ulemerero wa anthu okalamba ndiwo imvi zawo.+
32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.