Yobu 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa. Miyambo 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mvera bambo ako amene anakubereka,+ ndipo usanyoze mayi ako chifukwa chakuti akalamba.+ Maliro 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akalonga athu awapachika dzanja limodzi lokha.+ Anthuwo sanalemekezenso ngakhale amuna okalamba.+ 1 Timoteyo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usadzudzule mwamuna wachikulire mokalipa,+ koma umudandaulire ngati bambo ako. Amuna achinyamata uwadandaulire ngati abale ako,
6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa.
5 Usadzudzule mwamuna wachikulire mokalipa,+ koma umudandaulire ngati bambo ako. Amuna achinyamata uwadandaulire ngati abale ako,