Maliro 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akalonga athu anawapachika powamanga dzanja limodzi.+ Anthuwo sankalemekezanso amuna achikulire.+