Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 47:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+

      Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+

      Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+

      Koma iwe sunawachitire chifundo.+

      Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+

  • Yeremiya 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndadzazidwa ndi mkwiyo wa Yehova,

      Ndipo ndatopa ndi kuusunga.”+

      “Tsanulirani mkwiyowo pa mwana amene ali mumsewu,+

      Pa gulu la anyamata amene asonkhana pamodzi.

      Onse adzagwidwa, mwamuna limodzi ndi mkazi wake,

      Anthu achikulire limodzi ndi anthu okalamba.+

  • Maliro 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova wawabalalitsa+

      Ndipo sadzawakomeranso mtima.

      Anthu sadzalemekezanso ansembe+ kapena kuchitira chifundo amuna achikulire.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena