Maliro 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wawabalalitsa+ ndipo sadzawayang’ananso.+Anthu sadzaganiziranso ansembe.+ Sadzachitiranso chifundo amuna okalamba.”+
16 Yehova wawabalalitsa+ ndipo sadzawayang’ananso.+Anthu sadzaganiziranso ansembe.+ Sadzachitiranso chifundo amuna okalamba.”+