-
Mateyu 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma inu mumanena kuti, ‘Aliyense wouza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ine ndili nacho, chimene ndikanakuthandizirani, ndi mphatso yoperekedwa kwa Mulungu,”
-