Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake,+ aziphedwa ndithu.+ Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye mwini.+

  • Deuteronomo 27:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • Miyambo 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Wochitira zoipa bambo ake ndiponso wothamangitsa mayi ake,+ ndi mwana wochititsa manyazi ndi wonyozetsa.+

  • Miyambo 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense wotemberera bambo ake ndi mayi ake,+ nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+

  • Maliko 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anthu inu mumanena kuti, ‘Munthu akauza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ine ndili nacho, chimene mukanatha kupindula nacho, ndi khobani,+ (kutanthauza kuti, mphatso yoperekedwa+ kwa Mulungu,)”’ . . .

  • 2 Timoteyo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena