Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+

  • Ekisodo 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Wotemberera bambo ake ndi mayi ake aziphedwa ndithu.+

  • Levitiko 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Munthu akatemberera bambo ndi mayi ake,+ aziphedwa ndithu.+ Iye watemberera bambo ndi mayi ake. Mlandu wa magazi ake ukhale wa iye mwini.+

  • Deuteronomo 27:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • Miyambo 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Wochitira zoipa bambo ake ndiponso wothamangitsa mayi ake,+ ndi mwana wochititsa manyazi ndi wonyozetsa.+

  • 2 Timoteyo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena