Levitiko 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova. Tito 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna achikulire+ akhale osachita zinthu mopitirira malire, opanda chibwana,+ oganiza bwino, achikhulupiriro cholimba,+ achikondi chachikulu, ndi opirira+ kwambiri.
32 “‘Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzim’patsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.
2 Amuna achikulire+ akhale osachita zinthu mopitirira malire, opanda chibwana,+ oganiza bwino, achikhulupiriro cholimba,+ achikondi chachikulu, ndi opirira+ kwambiri.