Miyambo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Imvi ndizo chisoti chachifumu cha ulemerero+ zikapezeka m’njira yachilungamo.+ Miyambo 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukongola kwa anyamata ndiko mphamvu zawo,+ ndipo ulemerero wa anthu okalamba ndiwo imvi zawo.+