1 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+
8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+