1 Mafumu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru kwa akulu+ amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+ Yobu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?
6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru kwa akulu+ amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+
12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?