2 Samueli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Abisalomu anafunsa Ahitofeli kuti: “Amuna inu, nenani maganizo anu.+ Tichite chiyani?” Miyambo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.+ Koma pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+ Miyambo 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukongola kwa anyamata ndiko mphamvu zawo,+ ndipo ulemerero wa anthu okalamba ndiwo imvi zawo.+
14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.+ Koma pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+