2 Mbiri 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru+ kwa akulu amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+ Miyambo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+
6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru+ kwa akulu amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+
17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+