2 Samueli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Abisalomu anafunsa Ahitofeli kuti: “Amuna inu, nenani maganizo anu.+ Tichite chiyani?” Yobu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?
12 Kodi okalamba si paja amakhala ndi nzeru,+Ndipo amene akhala masiku ambiri si paja amamvetsa zinthu?