1 Mafumu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru kwa akulu+ amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+
6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu inafunsira nzeru kwa akulu+ amene anali kutumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Inawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”+