Deuteronomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+ Miyambo 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pakuti wondipeza ine, ndithu adzapezanso moyo+ ndipo Yehova adzasangalala naye,+ Miyambo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova kudzawonjezera masiku,+ koma zaka za anthu oipa zidzafupikitsidwa.+
2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+