Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+

  • Yoswa 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Tsopano opani Yehova+ ndi kum’tumikira mosalakwitsa ndiponso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje ndi ku Iguputo,+ ndipo tumikirani Yehova.

  • Yobu 28:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiyeno anauza munthu kuti,

      ‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+

      Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+

  • Salimo 111:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+

      ש [Sin]

      Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+

      ת [Taw]

      Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+

  • Salimo 128:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+

      Amene amayenda m’njira za Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena