Levitiko 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero asamaperekenso nsembe zawo ku ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ zimene akuchita nazo chiwerewere.+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, m’mibadwo yanu yonse.”’ Ezekieli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sanasiye zauhule zake zimene anachokera nazo ku Iguputo. Aiguputowo anagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ndiwo anatsamira chifuwa chake ali namwali ndipo anali kuchita naye zachiwerewere.+
7 Chotero asamaperekenso nsembe zawo ku ziwanda zooneka ngati mbuzi*+ zimene akuchita nazo chiwerewere.+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, m’mibadwo yanu yonse.”’
8 Iye sanasiye zauhule zake zimene anachokera nazo ku Iguputo. Aiguputowo anagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ndiwo anatsamira chifuwa chake ali namwali ndipo anali kuchita naye zachiwerewere.+