Levitiko 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho asamaperekenso nsembe zawo kwa ziwanda zooneka ngati mbuzi+ zimene akuzilambira.*+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, mʼmibadwo yanu yonse.”’
7 Choncho asamaperekenso nsembe zawo kwa ziwanda zooneka ngati mbuzi+ zimene akuzilambira.*+ Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale, mʼmibadwo yanu yonse.”’