Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Mateyu 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+
13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+