Luka 9:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Choncho anatsogoza amithenga. Iwo ananyamuka ndi kukalowa m’mudzi wa Asamariya,+ kukakonzekera kufika kwake. Luka 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+
52 Choncho anatsogoza amithenga. Iwo ananyamuka ndi kukalowa m’mudzi wa Asamariya,+ kukakonzekera kufika kwake.
32 Koma akaona kuti sangakwanitse, mwamsanga amatumiza akazembe kwa mfumu inayo isanafike pafupi, kukapempha mtendere.+