Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 46:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.

      Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+

  • Mateyu 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina,+ ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomezi+ m’malo osiyanasiyana.

  • Machitidwe 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndinu amene mwa mzimu woyera, munanena kudzera pakamwa pa kholo lathu Davide,+ mtumiki wanu kuti, ‘N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe, ndiponso n’chifukwa chiyani mitundu ya anthu ikusinkhasinkha zinthu zopanda pake?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena