Yoswa 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+ Amosi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye amasungunula dziko mwa kungolikhudza.+ Onse okhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonse lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.+
24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+
5 Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye amasungunula dziko mwa kungolikhudza.+ Onse okhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonse lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.+