Amosi 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa chifukwa chimenechi dziko lidzagwedezeka,+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonselo lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo ndi kuwinduka, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+
8 Pa chifukwa chimenechi dziko lidzagwedezeka,+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonselo lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo ndi kuwinduka, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.’+