Amosi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye amasungunula dziko mwa kungolikhudza.+ Onse okhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonse lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.+
5 Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa, ndiye amasungunula dziko mwa kungolikhudza.+ Onse okhala mmenemo adzalira.+ Dziko lonse lidzasefukira ngati mtsinje wa Nailo, ndipo kenako lidzaphwa ngati mtsinje wa Nailo wa ku Iguputo.+