15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi.
2 Taona! Mdima+ udzaphimba dziko lapansi, ndipo mdima wandiweyani udzaphimba mitundu ya anthu. Koma kuwala kwa Yehova kudzafika pa iwe, ndipo ulemerero wake udzaonekera pa iwe.+