Yesaya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+ Yesaya 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu a mu Iguputo adzadabwa kwambiri+ ndipo ine ndidzasokoneza zolinga za dzikolo.+ Iwo adzafunsira kwa milungu yopanda pake,+ kwa anthu amatsenga, kwa olankhula ndi mizimu ndiponso kwa olosera zam’tsogolo.+
10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+
3 Anthu a mu Iguputo adzadabwa kwambiri+ ndipo ine ndidzasokoneza zolinga za dzikolo.+ Iwo adzafunsira kwa milungu yopanda pake,+ kwa anthu amatsenga, kwa olankhula ndi mizimu ndiponso kwa olosera zam’tsogolo.+