Salimo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti akuchitirani zinthu zoipa.+Alinganiza kuchita zinthu zimene sangazikwanitse.+ Salimo 140:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, munthu woipa musam’patse zimene mtima wake umafuna.+Musalole kuti chiwembu chawo chitheke chifukwa angadzikweze.+ [Seʹlah.]
8 Inu Yehova, munthu woipa musam’patse zimene mtima wake umafuna.+Musalole kuti chiwembu chawo chitheke chifukwa angadzikweze.+ [Seʹlah.]