Salimo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+ Salimo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+
10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+
16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+