Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano Esitere anati: “Ngati zingakukomereni mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima,+ komanso ngati n’zoyenera kwa inu mfumu ndiponso ngati ndine munthu wabwino kwa inu, palembedwe makalata ofafaniza makalata+ achiwembu amene Hamani, mwana wa Hamedata Mwagagi,+ analemba pofuna kuwononga Ayuda+ amene ali m’zigawo zanu zonse mfumu.+

  • Esitere 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Moredekai analemba makalatawo m’dzina la Mfumu+ Ahasiwero ndi kuwadinda+ ndi mphete yodindira ya mfumu.+ Atatero anatumiza makalatawo kudzera mwa amtokoma okwera pamahatchi+ aliwiro amene anali kuwagwiritsa ntchito potumikira mfumu.

  • Esitere 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Esitere anati: “Ngati zingakukomereni mfumu,+ lolani kuti mawa Ayuda amene ali mu Susani achite mogwirizana ndi zimene lamulo laleroli likunena.+ Lolani kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena