Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+

  • Genesis 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero, Mulungu poyang’ana dziko lapansi anaona kuti laipa,+ chifukwa njira za anthu onse zinali zitaipa.+

  • Genesis 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno anati: “Tiyeni timange mzinda wathuwathu, ndipo nsanja yake ikafike m’mwamba mwenimweni.+ Tikatero tidzipangira dzina loti titchuke nalo,+ ndipo sitibalalikana padziko lonse lapansi.”+

  • Deuteronomo 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+

      Si ana ake, chilemacho n’chawo.+

      Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+

  • Yeremiya 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’

  • Maliko 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo anapitiriza kuwauza kuti: “Mochenjera, mumakankhira pambali malamulo+ a Mulungu kuti musunge mwambo wanu.

  • Yakobo 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma munthu aliyense amayesedwa mwa kukopedwa ndi kukodwa m’chilakolako chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena