Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, tikuona kuwala.+ Yeremiya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Chivumbulutso 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+
13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu, ndi wa Mwanawankhosa.+