Salimo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu anali kudalira inu.+Iwo anali kudalira inu ndipo munali kuwapulumutsa.+ Yeremiya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+ Yeremiya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+
8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+
7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+